
Apolisi amanga mayi wina kamba kogwedeza matako ku Ndirande
Apolisi amanga mayi wina, Comfort Hausi, yemwe anali akuchokera ku ntchito atasinthana naye mawu. Malingana ndi abale ake, Hausi anapatsidwa mpata kuti adutse pa Chinseu kulowera njira ya paChipiku ndipo wapolisi wina anamuuza kuti afulumire. Koma …